Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Eksodo 16:11 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

11 Yehova anati kwa Mose,

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

11 Ndipo Yehova ananena ndi Mose, ndi kuti,

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

11 Ndipo Yehova ananena ndi Mose, ndi kuti,

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

11 Chauta adauza Mose kuti,

Onani mutuwo Koperani




Eksodo 16:11
2 Mawu Ofanana  

Pamene Aaroni amayankhula ndi gulu lonse la Aisraeli, iwo anayangʼana ku chipululu, ndipo ulemerero wa Yehova umaoneka mu mtambo.


“Ine ndamva kudandaula kwa Aisraeli. Awuze kuti, ‘Madzulo mudzadya nyama ndipo mmawa mudzakhuta buledi. Pamenepo mudzadziwa kuti ine ndine Yehova Mulungu wanu.’ ”


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa