Eksodo 12:9 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Musadzadye yayiwisi kapena yophika, koma mudzawotche yonse, mutu, miyendo ndi zamʼmimba. Onani mutuwoBuku Lopatulika9 Musaidya yaiwisi, kapena yophika ndi madzi konse ai, koma yoocha pamoto; mutu wake ndi miyendo yake ndi matumbo ake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Musaidya yaiwisi, kapena yophika ndi madzi konse ai, koma yoocha pamoto; mutu wake ndi miyendo yake ndi matumbo ake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Musaidye yaiŵisi kapena yophika, koma muwotche yonse pamodzi ndi mutu wake womwe, miyendo ndi zonse zam'kati. Onani mutuwo |