Eksodo 12:44 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero44 Kapolo aliyense amene munagula angadye ngati atayamba wachita mdulidwe. Onani mutuwoBuku Lopatulika44 koma kapolo wa mwini aliyense, wogula ndi ndalama, utamdula, ndipo adyeko. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201444 koma kapolo wa mwini aliyense, wogula ndi ndalama, utamdula, ndipo adyeko. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa44 Kapolo aliyense wochita kugulidwa angadyeko, koma atayamba waumbalidwa. Onani mutuwo |