Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Eksodo 10:11 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

11 Ndakana! Amuna okha ndiwo apite ndi kukapembedza Yehova pakuti izi ndi zimene mwakhala mukupempha.” Kenaka Mose ndi Aaroni anathamangitsidwa pamaso pa Farao.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

11 Chotero ai, mukani tsopano, inu amuna aakulu, tumikirani Yehova pakuti ichi muchifuna. Ndipo anawapirikitsa pamaso pa Farao.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

11 Chotero ai, mukani tsopano, inu amuna akulu, tumikirani Yehova pakuti ichi muchifuna. Ndipo anawapirikitsa pamaso pa Farao.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

11 Ai! Inu, amuna nokhanu, ndiye mupite mukapembedze Chauta, popeza kuti ndi zimene mukufuna.” Atangomveka mau ameneŵa, Mose ndi Aroni adapirikitsidwa pamaso pa Farao.

Onani mutuwo Koperani




Eksodo 10:11
5 Mawu Ofanana  

Ngakhale odzikuza andipaka mabodza, ine ndimasunga malangizo anu ndi mtima wanga wonse.


Farao anati, “Yehova akhale ndi inu ngati ndingakuloleni kupita pamodzi ndi akazi ndi ana anu! Zikuoneka kuti mwakonzeka kuchita choyipa.


Farao anati kwa Mose, “Choka pamaso panga! Uwonetsetse kuti usadzaonekerenso pamaso panga! Tsiku limene ndidzakuonenso udzafa.”


Koma mfumu ya Igupto inati, “Mose ndi Aaroni, chifukwa chiyani mukuchititsa anthuwa kuti asagwire ntchito zawo? Bwererani ku ntchito zanu!”


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa