Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Afilipi 3:4 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

4 ngakhale kuti ineyo ndili ndi zifukwa zokwanira kudalira zinthu za thupizo. Ngati pali winanso amene akuganiza kuti ali ndi zifukwa zokwanira kudalira zinthu za thupi, ineyo ndili ndi zifukwa zoposa pamenepo.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

4 ndingakhale inenso ndili nako kakukhulupirira m'thupi; ngati wina yense ayesa kukhulupirira m'thupi, makamaka ineyu;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

4 ndingakhale inenso ndili nako kakukhulupirira m'thupi; ngati wina yense ayesa kukhulupirira m'thupi, makamaka ineyu;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

4 Komabetu ineyo ndikadatha kudalira miyambo yathupiyi. Ngati alipo wina woganiza kuti ali ndi chifukwa chodalira miyambo yathupi yotere, ineyo ndili ndi chifukwa choposa apo.

Onani mutuwo Koperani




Afilipi 3:4
4 Mawu Ofanana  

Choncho ganizirani mozama. Iye amene ali nazo adzapatsidwa zambiri, iye amene alibe, ngakhale chimene akuganiza kuti ali nacho adzalandidwa.”


Choncho, kuyambira tsopano mpaka mʼtsogolo ife sitiganizirapo za munthu aliyense monga mwanzeru za umunthu, ngakhale kuti poyamba tinkaganiza za Khristu mʼnjira imeneyi, koma tsopano sititeronso.


“Ife amene ndife Ayuda mwachibadwa, osati anthu a mitundu ina ochimwa,


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa