Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




2 Samueli 9:4 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

4 Mfumu inafunsa kuti, “Ali kuti?” Ziba anayankha kuti, “Iye ali ku nyumba ya Makiri mwana wa Amieli ku Lodebara.”

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

4 Ndipo mfumu inanena naye, Ali kuti iyeyo? Ziba nanena kwa mfumu, Onani ali m'nyumba ya Makiri mwana wa Amiyele ku Lodebara.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

4 Ndipo mfumu inanena naye, Ali kuti iyeyo? Ziba nanena kwa mfumu, Onani ali m'nyumba ya Makiri mwana wa Amiyele ku Lodebara.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

4 Mfumu idamufunsa kuti, “Ali kuti?” Ziba adayankha kuti, “Ali ku nyumba ya Makiri, mwana wa Amiyele, ku Lodebara.”

Onani mutuwo Koperani




2 Samueli 9:4
4 Mawu Ofanana  

ndipo anaona mʼbado wachitatu wa ana a Efereimu. Yosefe anatenganso ana a Makiri, mwana wa Manase kukhala ngati ana a mʼbanja lake.


Kotero mfumu inamubweretsa kuchokera ku Lodebara, ku nyumba ya Makiri mwana wa Amieli.


Inu amene mukunyadira kuti munagonjetsa Lo Debara ndipo mukunena kuti, “Kodi sitinatenge Karinaimu ndi mphamvu zathu zokha?”


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa