2 Samueli 22:5 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 “Mafunde a imfa anandizinga; mitsinje yothamanga yachiwonongeko inandiopsa kwambiri. Onani mutuwoBuku Lopatulika5 Pakuti mafunde a imfa anandizinga, mitsinje ya zopanda pake inandiopsa ine. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Pakuti mafunde a imfa anandizinga, mitsinje ya zopanda pake inandiopsa ine. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 “Zoŵaŵa za imfa zidandizinga, mitsinje ya ku malo a anthu akufa idandisefukira. Onani mutuwo |