Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




2 Samueli 19:2 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

2 Ndipo kwa asilikali onse chipambano cha tsiku limenelo chinasandulika maliro, chifukwa tsiku limenelo anthu anamva kuti mfumu ili pa chisoni chachikulu chifukwa cha mwana wake.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

2 Ndipo chipulumutso cha tsiku lija chinasandulika maliro kwa anthu onse; pakuti anthu anamva kuti, Mfumu ili ndi chisoni chifukwa cha mwana wake.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

2 Ndipo chipulumutso cha tsiku lija chinasandulika maliro kwa anthu onse; pakuti anthu anamva kuti, Mfumu ili ndi chisoni chifukwa cha mwana wake.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

2 Choncho chikondwerero cha tsikulo chidasanduka maliro kwa anthu onse, pakuti anthu adamva kuti mfumu ili pa chisoni chachikulu chifukwa cha mwana wake.

Onani mutuwo Koperani




2 Samueli 19:2
5 Mawu Ofanana  

Yowabu mwana wa Zeruya anadziwa kuti maganizo a mfumu ali pa Abisalomu.


Yowabu anawuzidwa kuti, “Mfumu ikulira maliro a Abisalomu.”


Ankhondo analowa mu mzinda mwakachetechete tsiku limenelo ngati momwe amalowera anthu mwamanyazi chifukwa athawa ku nkhondo.


Kuwala kwa nkhope ya mfumu kumapatsa moyo; ndipo kukoma mtima kwake kuli ngati mitambo ya mvula nthawi ya chilimwe.


Mkwiyo wa mfumu uli ngati kubangula kwa mkango, koma kukoma mtima kwake kuli ngati mame pa udzu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa