Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




2 Samueli 13:7 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

7 Davide anatumiza mawu kwa Tamara ku nyumba yaufumu kuti, “Pita ku nyumba ya mlongo wako Amnoni ndipo ukamukonzere chakudya.”

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

7 Ndipo Davide anatumiza mau kwao kwa Tamara, kuti, Upite kunyumba ya mlongo wako Aminoni, numkonzere chakudya.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

7 Ndipo Davide anatumiza mau kwao kwa Tamara, kuti, Upite kunyumba ya mlongo wako Aminoni, numkonzere chakudya.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

7 Davide adatumiza mau kwa Tamara kuti, “Upite kunyumba kwa mbale wako Aminoni, ukamphikire chakudya.”

Onani mutuwo Koperani




2 Samueli 13:7
3 Mawu Ofanana  

Kotero Amnoni anagona nakhala ngati akudwala. Mfumu itabwera kudzamuona, Amnoni anati kwa iyo, “Ine ndikufuna mlongo wanga Tamara kuti abwere adzandipangire buledi wapamwamba ineyo ndikuona, kuti ndidye ali mʼmanja mwake.”


Choncho Tamara anapitadi ku nyumba ya mlongo wake Amnoni kumalo kumene ankagona. Anakanda ufa, nawumba buledi Amunoniyo akuona ndipo anaphika bulediyo.


Davide atadzimangira nyumba zina mu Mzinda wa Davide, iye anakonza malo a Bokosi la Mulungu ndipo analimangira tenti.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa