Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




2 Samueli 13:16 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

16 Iye anayankha, “Ayi! Kundithamangitsa kukhala kulakwa kwakukulu kuposa zimene wachita kale kwa ine.” Koma anakana kumumvera.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

16 Koma iye ananena naye, Usamatero, pakuti choipa ichi chakuti ulikundipirikitsa nchachikulu choposa china chija unandichitira ine. Koma anakana kumvera.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

16 Koma iye ananena naye, Usamatero, pakuti choipa ichi chakuti ulikundipirikitsa nchachikulu choposa china chija unandichitira ine. Koma anakana kumvera.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

16 Koma Tamarayo adati, “Iyai, mlongo wanga, kundipirikitsa chotere nkulakwa koposa zimene wandichitazi.” Koma Aminoni sadafune kumva zimene ankanena Tamarazo.

Onani mutuwo Koperani




2 Samueli 13:16
2 Mawu Ofanana  

Atatero Amnoni anadana naye kwambiri. Iyeyo anamuda kuposa momwe anamukondera. Amnoni anati, “Dzuka ndipo tuluka!”


Amnoni anayitana wantchito wake ndipo anati, “Mutulutse mkazi uyu muno ndipo utseke chitseko akatuluka.”


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa