Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




2 Samueli 12:2 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

2 Munthu wolemerayo anali ndi nkhosa ndi ngʼombe zambiri,

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

2 Wolemerayo anali nazo zoweta zazing'ono ndi zazikulu zambiri ndithu;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

2 Wolemerayo anali nazo zoweta zazing'ono ndi zazikulu zambiri ndithu;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

2 Wolemerayo anali ndi nkhosa zambiri ndi ng'ombenso zambiri.

Onani mutuwo Koperani




2 Samueli 12:2
7 Mawu Ofanana  

Tsono Yehova anatumiza Natani kwa Davide. Atafika kwa Davide anati, “Panali anthu awiri mʼmizinda ina, wina wolemera ndi wina wosauka.


koma wosaukayo analibe chilichonse kupatula kankhosa kamodzi kakakazi kamene anakagula. Iye anakasunga ndipo kanakula naye pamodzi ndi ana ake. Kamadya chakudya chake, kamamwera chikho chake ndipo kamagona mʼmanja mwake. Kanali ngati mwana wamkazi kwa iyeyo.


Ndinakupatsanso banja la mbuye wako ndiponso akazi a mbuye wako mʼmanja mwako. Ine ndinakupatsanso banja la Israeli ndi Yuda. Ndipo ngati zinthu zonse izi zinali zochepa, Ine ndikanakupatsa zambiri.


Mfumu inanyamuka pamodzi ndi banja lake lonse. Koma iye anasiya azikazi khumi kuti azisamalira nyumba yaufumu.


ndipo anali ndi nkhosa 7,000, ngamira 3,000, ngʼombe zantchito 1,000 ndi abulu aakazi 500, ndiponso anali ndi antchito ambiri. Iye anali munthu wotchuka kwambiri pakati pa anthu onse a mʼmayiko a kummawa.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa