Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




2 Samueli 11:5 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

5 Mkaziyo anakhala woyembekezera ndipo anatumiza mawu kwa Davide kunena kuti, “Ine ndine woyembekezera.”

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

5 Ndipo mkaziyo anaima, natumiza munthu nauza Davide, kuti Ndili ndi pakati.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

5 Ndipo mkaziyo anaima, natumiza munthu nauza Davide, kuti Ndili ndi pakati.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

5 Kenaka ataona kuti waima, adatumiza mau kwa Davide kukamuuza kuti, “Inetu ndi mommuja, sindili bwino!”

Onani mutuwo Koperani




2 Samueli 11:5
4 Mawu Ofanana  

Ndipo Davide anatumiza mawu awa kwa Yowabu: “Nditumizire Uriya Mhiti.” Ndipo Yowabu anamutumiza kwa Davide.


Paja nsanje imachititsa mwini mkaziyo kukalipa, ndipo sadzachita chifundo pobwezera.


“ ‘Ngati munthu wachita chigololo ndi mkazi wa mnzake, mwamunayo pamodzi ndi mkaziyo ayenera kuphedwa.


Ngati munthu apezeka akugona ndi mkazi wa mwini wake, ayenera kuphedwa munthuyo pamodzi ndi mkazi yemwe wagona nayeyo. Muyenera kuchotsa zoyipa mu Israeli.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa