Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




2 Samueli 10:7 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

7 Davide atamva zimenezi, anatumiza Yowabu ndi gulu lonse la ankhondo amphamvu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

7 Ndipo pamene Davide anachimva, anatumiza Yowabu ndi khamu lonse la anthu amphamvu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

7 Ndipo pamene Davide anachimva, anatumiza Yowabu ndi khamu lonse la anthu amphamvu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

7 Davide atamva zimenezo, adatuma Yowabu ndi gulu lake lonse la ankhondo, amphamvu okhaokha.

Onani mutuwo Koperani




2 Samueli 10:7
4 Mawu Ofanana  

Aamoni atazindikira kuti amukwiyitsa kwambiri Davide, anakapeza ankhondo oyenda pansi aganyu okwanira 20,000 kuchokera ku Asiriya wa ku Beti Rehobu ndi Aramu-Zoba, komanso ankhondo 1,000 kwa mfumu Maaka ndiponso ankhondo 22,000 ochokera ku Tobu.


Aamoni anatuluka ndi kukhala mʼmizere ya nkhondo pa chipata cha mzinda wawo, pamene Aaramu a ku Aramu-Zoba ndi Rehobu ndi ankhondo a ku Tobu ndi Maaka anali kwa wokha ku malo wopanda mitengo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa