Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




2 Samueli 1:13 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

13 Davide anati kwa mnyamata amene anabweretsa uthengawo, “Iwe umachokera kuti?” Iye anayankha kuti, “Ine ndine mwana wa mlendo Mwamaleki.”

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

13 Ndipo Davide ananena ndi mnyamata wakumuuzayo, Kwanu nkuti? Nayankha, Ine ndine mwana wa mlendo, Mwamaleke.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

13 Ndipo Davide ananena ndi mnyamata wakumuuzayo, Kwanu nkuti? Nayankha, Ine ndine mwana wa mlendo, Mwamaleke.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

13 Tsono Davide adafunsa mnyamata wodzanena uja kuti, “Kodi iwe ndiwe wa kuti?” Iye adati, “Munthune ndine mwana wa mlendo, Mwamaleke.”

Onani mutuwo Koperani




2 Samueli 1:13
3 Mawu Ofanana  

Kenaka anabwerera napita ku Eni-Misipati (ku Kadesi), ndipo anagonjetsa dera lonse la Aamaleki, kuphatikizanso Aamori amene ankakhala ku Hazazoni Tamara.


Iye anandifunsa, “Iwe ndiwe yani?” Ine ndinayankha kuti, “Ndine Mwamaleki.”


Davide anafunsa kuti, “Kodi ndiwe yani, ndipo ukuchokera kuti?” Iye anayankha kuti, “Ine ndine Mwigupto, kapolo wa Mwamaleki. Mbuye wanga anandisiya nditayamba kudwala masiku atatu apitawo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa