2 Samueli 1:1 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Atamwalira Sauli, Davide anabwerako kumene anakagonjetsa Aamaleki ndipo anakakhala ku Zikilagi masiku awiri. Onani mutuwoBuku Lopatulika1 Ndipo kunali atamwalira Saulo, pamene Davide anabwera atawapha Aamaleke, ndipo Davide atakhala ku Zikilagi masiku awiri; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Ndipo kunali atamwalira Saulo, pamene Davide anabwera atawapha Aamaleke, ndipo Davide atakhala ku Zikilagi masiku awiri; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Saulo atamwalira, Davide adabwerako kumene adaakagonjetsa Aamaleke kuja, ndipo adakakhala ku Zikilagi masiku aŵiri. Onani mutuwo |