Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




1 Samueli 27:3 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

3 Davide anakhala ndi Akisi ku Gati pamodzi ndi ankhondo ake, aliyense ndi banja lake. Davide ali ndi akazi ake awiri, Ahinoamu wa ku Yezireeli ndi Abigayeli wa ku Karimeli, mkazi wamasiye wa Nabala.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

3 Ndipo Davide anakhala ndi Akisi ku Gati, iye ndi anthu ake, munthu yense ndi a pabanja pake, inde Davide ndi akazi ake awiri, Ahinowamu wa ku Yezireele, ndi Abigaile wa ku Karimele, mkazi wa Nabala.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

3 Ndipo Davide anakhala ndi Akisi ku Gati, iye ndi anthu ake, munthu yense ndi a pabanja pake, inde Davide ndi akazi ake awiri, Ahinowamu wa ku Yezireele, ndi Abigaile wa ku Karimele, mkazi wa Nabala.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

3 Adakhala ndi Akisi ku Gati, iyeyo pamodzi ndi anthu ake, aliyense ndi banja lake. Davide anali ndi akazi ake aŵiri, Ahinowamu wa ku Yezireele ndi Abigaile wa ku Karimele, mkazi wamasiye wa Nabala.

Onani mutuwo Koperani




1 Samueli 27:3
7 Mawu Ofanana  

Davide anatenganso anthu amene anali nawo aliyense ndi banja lake, ndipo anakakhala ku midzi ya ku Hebroni.


Dzina lake linali Nabala ndipo anali wa fuko la Kalebe. Dzina la mkazi wake linali Abigayeli. Anali mkazi wanzeru ndi wokongola, koma mwamuna wake, wa banja la Kalebe, anali wowuma mtima ndi wamwano pa zochita zake.


Sauli anamva kuti Davide wathawira ku Gati, ndipo sanamufunefunenso.


Davide ndi anthu ake atafika ku Zikilagi anapeza kuti mzindawo watenthedwa ndi moto ndipo akazi awo, ana awo, amuna ndi akazi atengedwa ukapolo.


Akazi awiri a Davide, Ahinoamu wa ku Yezireeli ndi Abigayeli mkazi wa Nabala wa ku Karimeli anatengedwanso.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa