1 Samueli 26:2 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Choncho Sauli ananyamuka pamodzi ndi ankhondo ake 3,000 napita ku chipululu cha Zifi kukafunafuna Davide ku chipululuko. Onani mutuwoBuku Lopatulika2 Ndipo Saulo ananyamuka, natsikira chipululu cha Zifi, ndi anthu zikwi zitatu a Israele osankhika, kukafuna Davide m'chipululu cha Zifi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Ndipo Saulo ananyamuka, natsikira chipululu cha Zifi, ndi anthu zikwi zitatu a Israele osankhika, kukafuna Davide m'chipululu cha Zifi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Saulo adanyamuka napita ku chipululu cha Zifi atatenga ankhondo 3,000 osankhidwa, kuti akafunefune Davide kuchipululuko. Onani mutuwo |