1 Samueli 1:4 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Tsiku lopereka nsembe likafika Elikana amapereka magawo a nsembeyo kwa mkazi wake Penina ndi kwa ana ake onse aamuna ndi aakazi. Onani mutuwoBuku Lopatulika4 Ndipo pofika tsiku lakuti Elikana akapereka nsembe, iye anapatsa Penina mkazi wake, ndi ana ake onse, aamuna ndi aakazi, gawo lao; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Ndipo pofika tsiku lakuti Elikana akapereka nsembe, iye anapatsa Penina mkazi wake, ndi ana ake onse, aamuna ndi aakazi, gawo lao; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Tsiku limene Elikana ankapereka nsembe, ankapatsako magawo a nsembeyo kwa mkazi wake Penina ndi kwa ana ake aamuna ndi aakazi. Onani mutuwo |