Zekariya 4:13 - Buku Lopatulika13 Ndipo anandiyankha, nati, Sudziwa kodi kuti nziyani izi? Ndipo ndinati, Iai, mbuyanga. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Ndipo anandiyankha, nati, Sudziwa kodi kuti nziyani izi? Ndipo ndinati, Iai, mbuyanga. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Iye adati, “Monga iwe zimenezi sukuzidziŵa?” Ine ndidayankha kuti, “Inde, mbuye wanga, sindikuzidziŵa.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Iye anandiyankha kuti, “Kodi iwe sukuzidziwa zimenezi?” Ine ndinati, “Ayi mbuye wanga.” Onani mutuwo |