Zekariya 14:13 - Buku Lopatulika13 Ndipo kudzali tsiku lomwelo, kuti chisokonezo chachikulu chochokera kwa Yehova chidzakhala pakati pao; ndipo adzagwira yense dzanja la mnzake; ndi dzanja lake lidzaukira dzanja la mnzake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Ndipo kudzali tsiku lomwelo, kuti chisokonezo chachikulu chochokera kwa Yehova chidzakhala pakati pao; ndipo adzagwira yense dzanja la mnzake; ndi dzanja lake lidzaukira dzanja la mnzake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Pa tsiku limenelo Chauta adzasokoneza anthu ndi mantha aakulu, mpaka aliyense adzagwira dzanja la mnzake, ndipo adzayamba kumenyana okhaokha. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Pa tsiku limenelo Yehova adzasokoneza anthu akuluakulu. Munthu aliyense adzagwira dzanja la mnzake, ndi kuyamba kumenyana okhaokha. Onani mutuwo |