Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Zekariya 12:14 - Buku Lopatulika

14 mabanja onse otsala, banja lililonse pa lokha, ndi akazi ao pa okha.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

14 mabanja onse otsala, banja lililonse pa lokha, ndi akazi ao pa okha.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

14 Mabanja onse otsala adzalira paokha, ndipo akazi aonso adzalira paokha.”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

14 ndiponso mafuko onse pamodzi ndi akazi awo.

Onani mutuwo Koperani




Zekariya 12:14
4 Mawu Ofanana  

Ukakhala wanzeru, si yakoyako nzeruyo? Ndipo ukanyoza udzasauka wekha.


Ndipo akupulumuka mwa iwo adzapulumuka, koma adzakhala kumapiri ngati njiwa za kuzigwa, onse akubuula, aliyense m'mphulupulu zake.


banja la nyumba ya Levi pa lokha, ndi akazi ao pa lokha; banja la Asimei pa okha, ndi akazi ao pa okha;


Tsiku lomwelo padzatsegukira nyumba ya Davide ndi okhala mu Yerusalemu kasupe wa kwa uchimo ndi chidetso.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa