Yoweli 3:15 - Buku Lopatulika15 Dzuwa ndi mwezi zada, ndi nyenyezi zibweza kuwala kwao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 Dzuwa ndi mwezi zada, ndi nyenyezi zibweza kuwala kwao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 Dzuŵa ndi mwezi zada, ndipo nyenyezi zaleka kuŵala. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 Dzuwa ndi mwezi zidzadetsedwa, ndipo nyenyezi sizidzawalanso. Onani mutuwo |