Yoswa 9:6 - Buku Lopatulika6 Ndipo zinamuka kwa Yoswa kumisasa ku Giligala, ndipo zinati kwa iye ndi kwa amuna a Israele, Tachokera dziko lakutali, chifukwa chake mupangane nafe. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Ndipo zinamuka kwa Yoswa kumisasa ku Giligala, niziti kwa iye ndi kwa amuna a Israele, Tachokera dziko lakutali, chifukwa chake mupangane nafe. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Tsono adapita kwa Yoswa ku zithando ku Giligala kuja, namuuza iyeyo pamodzi ndi Aisraele onse kuti, “Ife tachoka ku dziko lakutali, ndipo tikufuna kuti tichite nanu chipangano.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Ndipo anapita kwa Yoswa ku msasa ku Giligala ndikumuwuza kuti, pamodzi ndi Aisraeli onse, “Ife tachokera ku dziko lakutali, ndipo tikufuna kuti muchite mgwirizano ndi ife.” Onani mutuwo |