Yoswa 8:7 - Buku Lopatulika7 pamenepo muziuka m'molalira ndi kulowa m'mzinda; pakuti Yehova Mulungu wanu; adzaupereka m'manja mwanu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 pamenepo muziuka m'molalira ndi kulowa m'mudzi; pakuti Yehova Mulungu wanu; adzaupereka m'manja mwanu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Pamenepo tsono mudzatuluke kuja mudzakhale mutabisalaku, ndipo mudzalanda mzindawo. Chauta, Mulungu wanu, adzakupatsani mzinda umenewo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 inu mudzatuluke pamene mwabisalapo ndi kulanda mzindawo. Yehova Mulungu wanu adzakupatsani mzindawo. Onani mutuwo |