Yoswa 8:6 - Buku Lopatulika6 ndipo adzatuluka kutitsata mpaka tidawakokera asiyane ndi mzinda; pakuti adzanena, Atithawa pamaso pathu monga poyamba paja; nafenso tidzathawa pamaso pao; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 ndipo adzatuluka kutitsata mpaka tidawakokera asiyane ndi mudzi; pakuti adzanena, Atithawa pamaso pathu monga poyamba paja; nafenso tidzathawa pamaso pao; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Adzatithamangitsa motero, mpaka ife titaona kuti ali kutali ndi mzindawo, chifukwa iwowo azidzati, ‘Akutithaŵa monga kale lija.’ Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Iwo adzatithamangitsa mpaka titawakokera kutali ndi mzindawo, pakuti iwo adzati, ‘Akutithawa monga anachitira poyamba.’ Pamene ife tizidzathawa, Onani mutuwo |