Yoswa 8:5 - Buku Lopatulika5 ndipo ine, ndi anthu onse ali nane, tidzayandikira mzinda; ndipo kudzali, pamene atuluka kudzakomana nafe, monga poyamba paja, tidzathawa pamaso pao; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 ndipo ine, ndi anthu onse ali nane, tidzayandikira mudzi; ndipo kudzali, pamene atuluka kudzakomana nafe, monga poyamba paja, tidzathawa pamaso pao; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Anthu anga pamodzi ndi ine ndiye tidzayambe kuuputa mzindawo cha kumaso kwake. Tsono akadzangotuluka kuti alimbane nafe, ife tidzabwerera m'mbuyo, monga momwe tidachitira tsiku lina lija. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Ine ndi gulu langa lonse tikayamba kuwuputa mzindawu, ndipo akadzangotuluka kudzalimbana nafe, ife tidzawathawa monga tinachitira poyamba. Onani mutuwo |