Yoswa 8:11 - Buku Lopatulika11 Ndi anthu onse a nkhondo okhala naye anakwera, nayandikira nafika pamaso pa mzinda, namanga misasa kumpoto kwa Ai; koma pakati pa iye ndi Ai panali chigwa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Ndi anthu onse a nkhondo okhala naye anakwera, nayandikira nafika pamaso pa mudzi, namanga misasa kumpoto kwa Ai; koma pakati pa iye ndi Ai panali chigwa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Ankhondo omwe anali ndi iyeyo adatsogolako, nakamanga zithando chakumpoto kupenyana ndi chipata cha mzindawo. Pakati pa iwowo ndi mzinda wa Aiwo panali chigwa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Gulu lonse la nkhondo limene linali ndi iye linatsogolako ndi kukamanga zithando pafupi ndi mzindawo chakumpoto mopenyana nawo. Pakati pa iwo ndi mzindawo panali chigwa. Onani mutuwo |