Yoswa 8:10 - Buku Lopatulika10 Ndipo Yoswa analawira m'mamawa, nayesa anthu, nakwera, iye ndi akulu a Israele, pamaso pa anthu a ku Ai. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Ndipo Yoswa analawira m'mamawa, nayesa anthu, nakwera, iye ndi akulu a Israele, pamaso pa anthu a ku Ai. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 M'mamaŵa, Yoswa adadzuka naitana ankhondo ake onse. Tsono iyeyo ndi atsogoleri a Aisraele, adapita ku Ai. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Mmawa mwake, Yoswa anadzuka nayitana asilikali ake. Tsono iye pamodzi ndi akuluakulu a Aisraeli anatsogola kupita ku Ai. Onani mutuwo |