Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Yoswa 7:8 - Buku Lopatulika

8 Ndidzanenanji, Ambuye, Israele atabwerera m'mbuyo pamaso pa adani ao?

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

8 Ndidzanenanji, Ambuye, Israele atabwerera m'mbuyo pamaso pa adani ao?

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

8 Nanga ndinene chiyani tsopano, Chauta, poona kuti Aisraele athamangitsidwa ndi adani ao chotero?

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

8 Tsono Ambuye, ine ndinene chiyani, pakuti tsopano Israeli anathamangitsidwa ndi adani ake?

Onani mutuwo Koperani




Yoswa 7:8
8 Mawu Ofanana  

Ndipo tsopano, Mulungu wathu, tidzanenanji pambuyo pa ichi? Pakuti tasiya malamulo anu,


Mutibwereretsa kuthawa otisautsa, ndipo akudana nafe adzifunkhira okha.


Munapinditsa kukamwa kwake kwa lupanga lake, osamuimika kunkhondo.


Ndidzaima pa dindiro langa ndi kudziika palinga, ndipo ndidzayang'anira ndione ngati adzanenanji mwa ine, ngatinso ndidzamyankha chiyani pa choneneza changa.


Ndipo Yoswa anati, Ha! Ambuye, Yehova, mwaolotseranji anthu awa pa Yordani, kutipereka ife m'dzanja la Aamori, kutiononga ife? Mwenzi titalola ndi kukhala tsidya lija la Yordani!


Akadzamva ichi Akanani ndi okhala m'dziko onse, adzatizinga ndi kuduliratu dzina lathu padziko lapansi; ndipo mudzachitiranji dzina lanu lalikulu?


Ndipo pamene anthu anafika ku zithandozo, akulu a Israele anati, Yehova anatikanthiranji lero pamaso pa Afilisti? Tikadzitengere likasa la chipangano la Yehova ku Silo, kuti likabwera pakati pa ife, lidzatipulumutsa m'dzanja la adani athu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa