Yoswa 7:16 - Buku Lopatulika16 Ndipo Yoswa analawira mamawa, nayandikizitsa Israele, fuko ndi fuko; ndi fuko la Yuda linagwidwa; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Ndipo Yoswa analawira mamawa, nayandikizitsa Israele, fuko ndi fuko; ndi fuko la Yuda linagwidwa; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 M'maŵa mwake Yoswa adadzuka m'mamaŵa, natulutsa Aisraele onse fuko limodzilimodzi. Fuko la Yuda lidalozedwa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Mmawa mwake Yoswa anabweretsa Israeli fuko limodzilimodzi ndipo fuko la Yuda linalozedwa. Onani mutuwo |