Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Yoswa 5:8 - Buku Lopatulika

8 Ndipo kunali, atatha kudula mtundu wonse, anakhala m'malo mwao m'chigono mpaka adachira.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

8 Ndipo kunali, atatha kudula mtundu wonse, anakhala m'malo mwao m'chigono mpaka adachira.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

8 Kuumbalako kutatha, Aisraele onse ankangokhala m'zithandomo kudikira kuti zilonda zipole.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

8 Atamaliza kuchita mdulidwe uja, anthu onse anakakhala ku misasa yawo kudikira kuti zilonda zipole.

Onani mutuwo Koperani




Yoswa 5:8
3 Mawu Ofanana  

Ndipo panali tsiku lachitatu pamene anamva kuwawa, ana aamuna awiri a Yakobo, Simeoni ndi Levi, abale ake a Dina, anatenga wina lupanga lake wina lake, nalimbika mtima nalowa m'mzinda napha amuna onse.


Koma ana ao aamuna amene anawautsa m'malo mwao, iwowa Yoswa anawadula; popeza anakhala osadulidwa, pakuti sanawadule panjira.


Ndipo Yehova anati kwa Yoswa, Lero lino ndakukunkhunizirani mtonzo wa Ejipito. Chifukwa chake dzina la malowo analitcha Giligala kufikira lero lino.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa