Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Yoswa 5:12 - Buku Lopatulika

12 Koma m'mawa mwake mana analeka, atadya iwo tirigu wakhwimbi wa m'dziko; ndipo ana a Israele analibenso mana; koma anadya zipatso za dziko la Kanani chaka chomwe chija.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

12 Koma m'mawa mwake mana analeka, atadya iwo tirigu wakhwimbi wa m'dziko; ndipo ana a Israele analibenso mana; koma anadya zipatso za dziko la Kanani chaka chomwe chija.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

12 Zitangotero, mana uja adaleka kugwa, ndipo sadapezekenso pakati pa Aisraele. Kuyambira nthaŵi imeneyo adayamba kudya chakudya cha ku Kanani.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

12 Atangodya chakudya cha mʼdzikomo, mana anasiya kugwa, ndipo sanapezekenso. Kuyambira nthawi imeneyo Aisraeli anayamba kudya chakudya cha mʼdziko la Kanaani.

Onani mutuwo Koperani




Yoswa 5:12
9 Mawu Ofanana  

Ndipo ana a Israele anadya mana zaka makumi anai, kufikira atalowa dziko la midzi; anadya mana kufikira analowa malire a dziko la Kanani.


Wabwino asiyira zidzukulu zake cholowa chabwino; koma wochimwa angosungira wolungama chuma chake.


kudzali, pakudya inu mkate wa m'dzikolo, muzikwezera Yehova nsembe yokweza.


Ine ndinatuma inu kukamweta chimene simunagwirirapo ntchito: ena anagwira ntchito, ndipo inu mwalowa ntchito yao.


Ndipo m'mawa mwake atatha Paska, anadya tirigu wakhwimbi wa m'dziko, mikate yopanda chotupitsa ndi tirigu wokazinga tsiku lomwe lija.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa