Yoswa 4:8 - Buku Lopatulika8 Ndipo ana a Israele anachita monga Yoswa anawalamulira, nasenza miyala khumi ndi iwiri pakati pa Yordani, monga Yehova adalankhula ndi Yoswa, monga mwa kuwerenga kwa mafuko a ana a Israele; ndipo anaoloka nayo kunka kogona, naiika komweko. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Ndipo ana a Israele anachita monga Yoswa anawalamulira, nasenza miyala khumi ndi iwiri pakati pa Yordani, monga Yehova adalankhula ndi Yoswa, monga mwa kuwerenga kwa mafuko a ana a Israele; ndipo anaoloka nayo kunka kogona, naiika komweko. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Anthuwo adachitadi zonse zimene Yoswa adaŵalamula. Adanyamula miyala khumi ndi iŵiri pakati pa mtsinje wa Yordani, monga momwe Chauta adalamulira Yoswa. Anthu a fuko lililonse la Aisraele adanyamula mwala umodzi. Miyalayo adapita nayo kukaikhazika pansi pamalo pamene panali zithando paja. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Aisraeli anachitadi monga Yoswa anawalamulira. Iwo ananyamula miyala khumi ndi iwiri kuchokera pakati pa Yorodani, fuko lililonse la Israeli mwala wake, monga Yehova analamulira Yoswa. Miyalayo anapita nayo ku misasa yawo nakayikhazika kumeneko. Onani mutuwo |