Yoswa 4:16 - Buku Lopatulika16 Lamulira ansembe akusenza likasa la umboni, kuti akwere kutuluka mu Yordani. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Lamulira ansembe akusenza likasa la umboni, kuti akwere kutuluka m'Yordani. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 “Lamula ansembe onyamula Bokosi lachipanganowo, kuti atuluke m'madzimo.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 “Lamula ansembe onyamula Bokosi la Chipanganowo kuti atuluke mu Yorodani.” Onani mutuwo |