Yoswa 4:10 - Buku Lopatulika10 Pakuti ansembe akusenza likasa anaima pakati pa Yordani, mpaka zitatha zonse Yehova adazilamulira Yoswa anene kwa anthu, monga mwa zonse Mose adalamulira Yoswa; ndipo anthu anafulumira kuoloka. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Pakuti ansembe akusenza likasa anaima pakati pa Yordani, mpaka zitatha zonse Yehova adazilamulira Yoswa anene kwa anthu, monga mwa zonse Mose adalamulira Yoswa; ndipo anthu anafulumira kuoloka. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Ansembe aja adaimirirabe pakati pa mtsinje wa Yordani, mpaka zitatha zonse zimene Chauta adaalamula Yoswa kuti auze anthu. Zimenezi ndizo zimene Mose anali atafotokozera Yoswa. Tsono anthu adaoloka mtsinjewo mofulumira. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Ansembe onyamula Bokosi lija anayimirirabe pakati pa Yorodani mpaka zonse zimene Yehova analamulira Yoswa kuti awuze anthu zinatha. Zimenezi zinali monga momwe Mose anamufotokozera Yoswa. Tsono anthu anawoloka mtsinjewo mofulumira. Onani mutuwo |