Yoswa 24:3 - Buku Lopatulika3 Ndipo ndinamtenga kholo lanu Abrahamu tsidya lija la mtsinje, ndi kumuyendetsa m'dziko lonse la Kanani ndi kuchulukitsa mbeu zake ndi kumpatsa Isaki. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Ndipo ndinamtenga kholo lanu Abrahamu tsidya lija la mtsinje, ndi kumuyendetsa m'dziko lonse la Kanani ndi kuchulukitsa mbeu zake ndi kumpatsa Isaki. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Tsono Abrahamuyo ndidamtenga ndi kumchotsa m'dzikomo patsidya pa Yufurate, ndipo ndidamtsogoza kupita naye ku dziko la Kanani. Ndidampatsa zidzukulu zambiri. Ndidampatsa Isaki, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Koma ine ndinatenga kholo lanu Abrahamu kumuchotsa ku dziko la kutsidya kwa mtsinje wa Yufurate ndipo ndinamutsogolera kupita ku dziko la Kanaani. Ndinamupatsa zidzukulu zambiri. Ndinamupatsa Isake, Onani mutuwo |