Yoswa 22:3 - Buku Lopatulika3 simunasiye abale anu masiku awa ambiri mpaka lero lino, koma mwasunga chisungire lamulo la Yehova Mulungu wanu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 simunasiya abale anu masiku awa ambiri mpaka lero lino, koma mwasunga chisungire lamulo la Yehova Mulungu wanu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Aisraele anzanu simudaŵasiye nthaŵi yonseyi mpaka lero lino. Mwasamaladi malamulo onse a Chauta, Mulungu wanu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Aisraeli anzanu simunawasiye nthawi yayitali yonseyi mpaka lero lino. Inu mwaonetsetsa kuti mwachita zonse zimene Yehova anakulamulani. Onani mutuwo |