Yoswa 22:2 - Buku Lopatulika2 nanena nao, Mwasunga inu zonsezo anakulamulirani Mose mtumiki wa Yehova; mwamveranso mau anga m'zonse ndinakulamulirani inu; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 nanena nao, Mwasunga inu zonsezo anakulamulirani Mose mtumiki wa Yehova; mwamveranso mau anga m'zonse ndinakulamulirani inu; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Ndipo adaŵauza kuti, “Zonse zimene Mose mtumiki wa Chauta adakulamulani kuti muchite, mwachitadi, ndipo mwamvera malamulo anga onse. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 ndipo anawawuza kuti, “Inu mwachita zonse zimene Mose mtumiki wa Yehova anakulamulani, ndipo mwamvera mu zonse zimene ndinakulamulirani. Onani mutuwo |