Yoswa 22:1 - Buku Lopatulika1 Pamenepo Yoswa anaitana Arubeni ndi Agadi, ndi hafu la fuko la Manase, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Pamenepo Yoswa anaitana Arubeni ndi Agadi, ndi fuko la Manase logawika pakati, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Pambuyo pake Yoswa adaitana anthu a fuko la Rubeni ndi la Gadi, ndi hafu lina lija la fuko la Manase wakuvuma. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Pambuyo pake Yoswa anayitanitsa fuko la Rubeni, fuko la Gadi ndi theka la fuko la Manase, Onani mutuwo |