Yoswa 21:9 - Buku Lopatulika9 Ndipo anapatsa motapa pa fuko la ana a Yuda, ndi pa fuko la ana a Simeoni, mizinda iyi yotchulidwa maina ao; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Ndipo anapatsa motapa pa fuko la ana a Yuda, ndi pa fuko la ana a Simeoni, midzi iyi yotchulidwa maina ao; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Mizinda ya Yuda ndi Simeoni imene idapatsidwa Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Awa ndi mayina a mizinda ya mafuko a Yuda ndi Simeoni imene inaperekedwa kwa zidzukulu za Aaroni, Onani mutuwo |