Yoswa 21:3 - Buku Lopatulika3 Ndipo ana a Israele anapatsa Alevi, kutapa pa cholowa chao, monga mwa lamulo la Yehova, mizinda iyi ndi mabusa ao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Ndipo ana a Israele anapatsa Alevi, kutapa pa cholowa chao, monga mwa lamulo la Yehova, midzi iyi ndi mabusa ao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Motero Aisraele adapatsa Aleviwo mizindayo pochita maere, pamodzi ndi mabusa a zoŵeta, kuchokera pa magawo ao omwewo, potsata zomwe Chauta adalamula. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Choncho, Aisraeli anapereka kwa fuko la Levi mizinda iyi pamodzi ndi malo owetera ziweto zawo kuchokera ku madera awo, monga Yehova analamulira: Onani mutuwo |