Yoswa 21:2 - Buku Lopatulika2 nanena nao ku Silo m'dziko la Kanani, ndi kuti Yehova analamulira mwa dzanja la Mose kuti atipatse mizinda yokhalamo ife, ndi mabusa a zoweta zathu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 nanena nao ku Silo m'dziko la Kanani, ndi kuti Yehova analamulira mwa dzanja la Mose kuti atipatse midzi yokhalamo ife, ndi mabusa a zoweta zathu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Aleviwo adafika ku Silo m'dziko la Kanani, nanena kuti, “Chauta adalamula kudzera mwa Mose kuti ife atipatse mizinda yokhalamo, ndiponso atipatse mabusa pozungulira mizindayo, kuti tizidyetsapo zoŵeta zathu.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 ku Silo mʼdziko la Kanaani ndipo anati, “Yehova analamula kudzera mwa Mose kuti atipatse mizinda kuti tikhalemo, pamodzi ndi malo odyetseramo ziweto zathu.” Onani mutuwo |