Yoswa 20:5 - Buku Lopatulika5 Ndipo akamlondola wolipsa mwazi, asampereke m'dzanja lake wakupha mnzakeyo; pakuti anakantha mnansi wake mosadziwa, osamuda kale. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Ndipo akamlondola wolipsa mwazi, asampereke m'dzanja lake wakupha mnzakeyo; pakuti anakantha mnansi wake mosadziwa, osamuda kale. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Munthu wofuna kulipsirayo akamlondola komweko, anthu amumzindamo asampereke munthu wopha mnzakeyo. Koma amtchinjirize chifukwa adachita zimenezo mwangozi, pakupha Mwisraele mnzake. Sadachite zimenezo mwachiwembu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Ngati munthu wolipsirayo amutsatira komweko atsogoleriwo asapereke munthu wakuphayo chifukwa anapha Mwisraeli mnzakeyo mosazindikira, osati mwachiwembu. Onani mutuwo |