Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Yoswa 20:2 - Buku Lopatulika

2 Nena ndi ana a Israele ndi kuti, Mudziikire mizinda yopulumukirako, monga ndinanena kwa inu mwa dzanja la Mose.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

2 Nena ndi ana a Israele ndi kuti, Mudziikire midzi yopulumukirako, monga ndinanena kwa inu mwa dzanja la Mose.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

2 “Uza Aisraele kuti, ‘Sankhulani mizinda yopulumukiramo, imene Ine ndidakuuzani kudzera mwa Mose.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

2 “Uza Aisraeli kuti apatule mizinda yopulumukiramo, monga ine ndinakulangizira kudzera mwa Mose,

Onani mutuwo Koperani




Yoswa 20:2
10 Mawu Ofanana  

Ndipo midziyo muipereke kwa Alevi ndiyo mizinda ija isanu ndi umodzi yopulumukirako; imene muipereke kuti wakupha mnzake athawireko; ndipo pamodzi ndi iyi muperekenso midzi makumi anai ndi iwiri.


Chifukwa chake tsopano iwo akukhala mwa Khristu Yesu alibe kutsutsidwa.


Ndipo Yehova anati kwa Yoswa,


Kuti athawireko wakupha munthu osamupha dala, osadziwa; ndipo idzakhalire inu yopulumukirako, kumpulumuka wolipsa mwazi.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa