Yoswa 2:16 - Buku Lopatulika16 Ndipo anati kwa iwo, Mukani kuphiri, olondola angakupezeni; mubisale kumeneko masiku atatu, mpaka atabwerera olondolawo, pamenepo muyende ulendo wanu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Ndipo anati kwa iwo, Mukani kuphiri, olondola angakupezeni; mubisale kumeneko masiku atatu, mpaka atabwerera olondolawo, pamenepo muyende ulendo wanu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Anali ataŵauza kuti, “Pitani mudzere kumapiriko, kuti otumidwa ndi mfumu aja angakupezeni. Papite masiku atatu mukubisalabe, mpaka iwowo atachokako. Zitatero tsono, mungathe kumapita.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Iye anawawuza kuti, “Pitani ku mapiri kuti okuthamangiraniwo asakupezeni. Mukabisale kumeneko masiku atatu mpaka iwo atabwerera, ndipo kenaka muzikapita kwanu.” Onani mutuwo |