Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Yoswa 2:13 - Buku Lopatulika

13 kuti mudzawasunga ndi moyo atate wanga ndi mai wanga, ndi alongo anga ndi abale anga, ndi zonse ali nazo, ndi kupulumutsa miyoyo yathu kuimfa.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

13 kuti mudzawasunga ndi moyo atate wanga ndi mai wanga, ndi alongo anga ndi abale anga, ndi zonse ali nazo, ndi kupulumutsa miyoyo yathu kuimfa.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

13 Bambo wanga, mai wanga, pamodzi ndi alongo anga, abale anga ndi mabanja ao omwe, tonsefe mudzatisungire moyo, musadzatiphe.”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

13 Inu mulonjeze kuti simudzapha abambo anga ndi amayi anga, abale anga ndi alongo anga ndi mabanja awo omwe.”

Onani mutuwo Koperani




Yoswa 2:13
3 Mawu Ofanana  

Ndipo tsopano, mundilumbiriretu kwa Yehova, popeza ndakuchitirani chifundo, kuti inunso mudzachitira chifundo a m'nyumba ya atate wanga ndi kundipatsa chizindikiro choona,


Ndipo amunawo anati kwa iye, Moyo wathu ndiwo moyo wanu, mukapanda kuwulula chodzera ife; ndipo kudzakhala kuti, pakutipatsa ife dziko ili Yehova, tidzakuchitira chifundo ndi choonadi.


Pamenepo anyamata ozondawo analowa, natulutsa Rahabi, ndi atate wake ndi mai wake ndi abale ake, ndi onse anali nao; anatulutsanso achibale ake onse; nawaika kunja kwa chigono cha Israele.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa