Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Yoswa 19:6 - Buku Lopatulika

6 ndi Betelebaoti, ndi Saruheni; mizinda khumi ndi itatu ndi midzi yao;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

6 ndi Betelebaoti, ndi Saruheni; midzi khumi ndi itatu ndi milaga yao;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

6 Betelebaoti ndiponso Saruheni. Yonse inalipo mizinda 13, pamodzi ndi midzi yake.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

6 Beti-Lebaoti ndi Saruheni. Yonse pamodzi inali mizinda 13 ndi midzi yawo.

Onani mutuwo Koperani




Yoswa 19:6
3 Mawu Ofanana  

ndi Lebaoti, ndi Silihimu, ndi Aini ndi Rimoni; mizinda yonse ndiyo makumi awiri kudza isanu ndi inai; pamodzi ndi midzi yao.


ndi Zikilagi, ndi Betemara-Kaboti, ndi Hazara-Susa:


Aini, Rimoni ndi Eteri ndi Asani; mizinda inai ndi midzi yao;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa