Yoswa 19:16 - Buku Lopatulika16 Ichi ndi cholowa cha ana a Zebuloni monga mwa mabanja ao, mizinda iyi ndi midzi yao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Ichi ndi cholowa cha ana a Zebuloni monga mwa mabanja ao, midzi iyi ndi milaga yao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Mizinda imeneyi pamodzi ndi midzi yake inali m'dziko limene mabanja a fuko la Zebuloni adalandira ngati choloŵa chao. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Mizinda imeneyi pamodzi ndi midzi yake ndi imene mabanja a fuko la Zebuloni analandira. Onani mutuwo |