Yoswa 19:12 - Buku Lopatulika12 ndi kuchokera ku Saridi anazungulira kunka kum'mawa kumatulukira dzuwa, mpaka malire a Kisiloti-Tabori; natuluka kunka ku Daberati, nakwera ku Yafiya; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 ndi kuchokera ku Saridi anazungulira kunka kum'mawa kumatulukira dzuwa, mpaka malire a Kisiloti-Tabori; natuluka kunka ku Daberati, nakwera ku Yafiya; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Pa mbali ina ya Saridi adapita chakuvuma ku malire a Kisiloti-Tabori, mpaka ku Debarati, nakafika ku Yafiya. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Kuchokera ku mbali ina ya Saridi malire anakhota kupita kummawa ku malire a Kisiloti-Tabori mpaka ku Daberati nakwera mpaka ku Yafiya. Onani mutuwo |