Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Yoswa 19:11 - Buku Lopatulika

11 nakwera malire ao kunka kumadzulo ndi ku Mareyala nafikira ku Dabeseti, nafikira ku mtsinje wa patsogolo pa Yokoneamu;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

11 nakwera malire ao kunka kumadzulo ndi ku Mareyala nafikira ku Dabeseti, nafikira ku mtsinje wa patsogolo pa Yokoneamu;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

11 Tsono malirewo adakwera naloŵa kuzambwe ku Mareyala, nakafika ku Debeseti ndi ku mtsinje wa kuvuma kwa Yokoneamu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

11 Malirewo anakwera kupita cha kumadzulo ku Marala nakafika ku Dabeseti ndi ku mtsinje wa kummawa kwa Yokineamu.

Onani mutuwo Koperani




Yoswa 19:11
5 Mawu Ofanana  

Baana mwana wa Ahiludi ku Taanaki ndi Megido ndi Beteseani konse, ali pafupi ndi Zaretani kunsi kwa Yezireele, kuyambira ku Beteseani kufikira ku Abele-Mehola, kufikiranso kundunji ku Yokomeamu;


ndi Yokomeamu ndi mabusa ake, ndi Betehoroni ndi mabusa ake,


mfumu ya ku Kedesi, imodzi; mfumu ya ku Yokoneamu ku Karimele, imodzi;


Ndipo maere achitatu anakwerera ana a Zebuloni monga mwa mabanja ao; ndi malire a cholowa chao anafikira ku Saridi;


ndi kuchokera ku Saridi anazungulira kunka kum'mawa kumatulukira dzuwa, mpaka malire a Kisiloti-Tabori; natuluka kunka ku Daberati, nakwera ku Yafiya;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa